Levitiko 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndidzaika chihema changa chopatulika pakati panu,+ ndipo sindidzanyansidwa nanu.+ Yesaya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Moyo wanga ukudana ndi masiku anu okhala mwezi ndi zikondwerero zanu.+ Zimenezi zasanduka katundu wolemera kwa ine,+ ndipo ndatopa kuzinyamula.+ Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
14 Moyo wanga ukudana ndi masiku anu okhala mwezi ndi zikondwerero zanu.+ Zimenezi zasanduka katundu wolemera kwa ine,+ ndipo ndatopa kuzinyamula.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+