Levitiko 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Yesaya 40:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mmisiri wapanga chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Mmisiri wina wa zitsulo wachikuta ndi golide,+ ndipo akuchipangira matcheni asiliva.+ Habakuku 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+
4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
19 Mmisiri wapanga chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Mmisiri wina wa zitsulo wachikuta ndi golide,+ ndipo akuchipangira matcheni asiliva.+
18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+