Genesis 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nawa tsopano mafumu aakulu amene analamulira dziko la Edomu,+ ana a Isiraeli asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse:+ Deuteronomo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+ Oweruza 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndipo m’masiku amenewo fuko la Dani+ linali kufuna cholowa chake kuti likakhale kumeneko, chifukwa mpaka pa nthawi imeneyi linali lisanalandirebe cholowa pakati pa mafuko onse a Isiraeli.+
31 Nawa tsopano mafumu aakulu amene analamulira dziko la Edomu,+ ana a Isiraeli asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse:+
5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+
18 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndipo m’masiku amenewo fuko la Dani+ linali kufuna cholowa chake kuti likakhale kumeneko, chifukwa mpaka pa nthawi imeneyi linali lisanalandirebe cholowa pakati pa mafuko onse a Isiraeli.+