Levitiko 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda m’dziko lanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wovutika+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’” Rute 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsiku lina Rute mkazi wachimowabu uja anapempha Naomi kuti: “Chonde ndiloleni ndipite kuminda ndikakunkhe+ balere m’mbuyo mwa aliyense amene angandikomere mtima.” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.”
22 “‘Mukamakolola zinthu za m’munda m’dziko lanu, musamachotseretu zonse m’mphepete mwa mundawo, ndipo musamachite khunkha m’munda mwanumo.+ Zotsalazo muzisiyira wovutika+ ndi mlendo wokhala pakati panu.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
2 Tsiku lina Rute mkazi wachimowabu uja anapempha Naomi kuti: “Chonde ndiloleni ndipite kuminda ndikakunkhe+ balere m’mbuyo mwa aliyense amene angandikomere mtima.” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.”