Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho moyo wake ulibe chilichonse.+ Koma anthu akhama adzanenepa.+ Miyambo 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye amayang’anira zochitika za pabanja pake, ndipo sadya chakudya cha ulesi.+ Miyambo 31:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 M’patseni zipatso za manja ake,+ ndipo ntchito zake zimutamande ngakhale m’zipata.+ 1 Atesalonika 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.
11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.