-
1 Samueli 20:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Anandiuza kuti, ‘Chonde ndilole ndipite kumzinda wakwathu kukapereka nsembe ya banja lathu. M’bale wanga ndi amene wandiitanitsa. Choncho ngati ungandikomere mtima, chonde ndilole ndichoke mwakachetechete ndiponso mofulumira kuti ndikaone abale anga.’ N’chifukwa chake sanabwere kudzadya chakudya pamodzi ndi mfumu.”
-