Deuteronomo 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yehova adzakulanga ndi misala,+ khungu+ ndipo adzakuchititsa kudabwa kwambiri.+ Salimo 102:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga wawauka ngati udzu ndipo wauma,+Pakuti ndilibe chilakolako chofuna kudya chakudya.+ Salimo 143:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga+ walefuka,Ndipo wachita dzanzi.+