Yoswa 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Yoswa anadalitsa Kalebe mwana wa Yefune, ndi kum’patsa mzinda wa Heburoni monga cholowa chake.+ 2 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+
13 Pamenepo Yoswa anadalitsa Kalebe mwana wa Yefune, ndi kum’patsa mzinda wa Heburoni monga cholowa chake.+
2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+