Salimo 85:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzamvetsera zimene Mulungu woona Yehova adzanena,+Pakuti adzanena za mtendere kwa anthu ake+ ndi kwa okhulupirika ake.Koma iwo asadzidalire kwambiri ngati kale.+ Yesaya 55:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 N’chifukwa chiyani anthu inu mukuwononga ndalama polipirira zinthu zimene si chakudya, ndipo n’chifukwa chiyani mukuvutika kugwirira ntchito zinthu zimene sizikhutitsa?+ Tcherani khutu kwa ine kuti mudye zabwino,+ ndiponso kuti moyo wanu usangalale kwambiri ndi zakudya zamafuta.+ Danieli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anandiuza kuti: “Iwe munthu wokondedwa kwambiri,+ usachite mantha.+ Mtendere ukhale nawe.+ Limba mtima, ndithu, limba mtima.”+ Atangolankhula nane, ndinadzilimbitsa ndipo pamapeto pake ndinati: “Lankhulani mbuyanga+ chifukwa inu mwandilimbikitsa.”+
8 Ndidzamvetsera zimene Mulungu woona Yehova adzanena,+Pakuti adzanena za mtendere kwa anthu ake+ ndi kwa okhulupirika ake.Koma iwo asadzidalire kwambiri ngati kale.+
2 N’chifukwa chiyani anthu inu mukuwononga ndalama polipirira zinthu zimene si chakudya, ndipo n’chifukwa chiyani mukuvutika kugwirira ntchito zinthu zimene sizikhutitsa?+ Tcherani khutu kwa ine kuti mudye zabwino,+ ndiponso kuti moyo wanu usangalale kwambiri ndi zakudya zamafuta.+
19 Iye anandiuza kuti: “Iwe munthu wokondedwa kwambiri,+ usachite mantha.+ Mtendere ukhale nawe.+ Limba mtima, ndithu, limba mtima.”+ Atangolankhula nane, ndinadzilimbitsa ndipo pamapeto pake ndinati: “Lankhulani mbuyanga+ chifukwa inu mwandilimbikitsa.”+