Yesaya 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+ 2 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi, n’kutembenukira ku nkhani zonama.+ Aheberi 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musatengeke ndi ziphunzitso zosiyanasiyana zachilendo.+ Ndi bwino kuti mtima ukhale wolimba chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu,+ osati chifukwa cha zakudya.+ Pakuti amene amatanganidwa ndi zakudyazo sakupindula nazo.
7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+
9 Musatengeke ndi ziphunzitso zosiyanasiyana zachilendo.+ Ndi bwino kuti mtima ukhale wolimba chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu,+ osati chifukwa cha zakudya.+ Pakuti amene amatanganidwa ndi zakudyazo sakupindula nazo.