Aroma 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ufumu wa Mulungu+ si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo,+ mtendere+ ndi chimwemwe+ zobwera ndi mzimu woyera. 1 Akorinto 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma chakudya sichingatikometse pamaso pa Mulungu.+ Ngati sitinadye chakudyacho, sikuti tamulakwira, ndiponso ngati tadya, sikuti tamukondweretsa mwapadera.+ Akolose 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho munthu asakuweruzeni+ pa nkhani ya kudya ndi kumwa+ kapena chikondwerero chinachake,+ kapenanso kusunga tsiku lokhala mwezi,+ ngakhalenso kusunga sabata,+
17 Pakuti ufumu wa Mulungu+ si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo,+ mtendere+ ndi chimwemwe+ zobwera ndi mzimu woyera.
8 Koma chakudya sichingatikometse pamaso pa Mulungu.+ Ngati sitinadye chakudyacho, sikuti tamulakwira, ndiponso ngati tadya, sikuti tamukondweretsa mwapadera.+
16 Choncho munthu asakuweruzeni+ pa nkhani ya kudya ndi kumwa+ kapena chikondwerero chinachake,+ kapenanso kusunga tsiku lokhala mwezi,+ ngakhalenso kusunga sabata,+