Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo iye anauza Abulamu kuti: “Unditengere ng’ombe ya zaka zitatu yomwe sinaberekepo, mbuzi yaikazi ya zaka zitatu, nkhosa yamphongo ya zaka zitatu, ndiponso njiwa yaing’ono ndi mwana wa nkhunda.”+

  • 1 Samueli 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho pangani ngolo+ yatsopano, ndipo mutenge ng’ombe ziwiri zoyamwitsa zimene sizinanyamulepo goli+ ndi kuzimangirira kungoloyo. Ana a ng’ombezo muwabweze kunyumba kuti asatsatire amayi awo.

  • 1 Samueli 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma Samueli anati: “Ndipita bwanji? Sauli akangomva andipha ndithu.”+ Atatero, Yehova anamuuza kuti: “Popita utenge ng’ombe yaikazi yaing’ono pakati pa ng’ombe zako, ndipo ukanene kuti, ‘Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena