Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zitatero, anthu onse anayamba kuuza Samueli kuti: “Pempherera+ atumiki ako kwa Yehova Mulungu wako, chifukwa sitikufuna kufa. Pakuti tawonjeza choipa china pa machimo athu onse, mwa kupempha kuti tikhale ndi mfumu.”

  • Salimo 78:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+

      Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+

  • Salimo 86:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pa tsiku la nsautso yanga ndidzaitana pa inu,+

      Ndipo inu mudzandiyankha.+

  • Yesaya 37:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mwina Yehova Mulungu amva mawu onse a Rabisake,+ amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamutuma, kuti adzatonze+ nawo Mulungu wamoyo. Ndipo mwina amulanga chifukwa cha mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva.+ Inuyo mupereke pemphero+ m’malo mwa otsalira amene alipo.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena