1 Samueli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Samueli anawauza kuti: “Sonkhanitsani Aisiraeli onse+ pamodzi ku Mizipa,+ kuti ndikupempherereni+ kwa Yehova.” 1 Samueli 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso, n’zosatheka kuti ineyo ndichimwire Yehova mwa kusiya kukupemphererani.+ Ndipo ndiyenera kukulangizani+ za njira yabwino+ ndi yolondola. Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+ Machitidwe 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poyankha Simoni uja anati: “Amuna inu, ndipemphereni chonde kwa Yehova mopembedzera+ kuti zonse mwanenazo zisandigwere.” Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
5 Ndiyeno Samueli anawauza kuti: “Sonkhanitsani Aisiraeli onse+ pamodzi ku Mizipa,+ kuti ndikupempherereni+ kwa Yehova.”
23 Komanso, n’zosatheka kuti ineyo ndichimwire Yehova mwa kusiya kukupemphererani.+ Ndipo ndiyenera kukulangizani+ za njira yabwino+ ndi yolondola.
24 Poyankha Simoni uja anati: “Amuna inu, ndipemphereni chonde kwa Yehova mopembedzera+ kuti zonse mwanenazo zisandigwere.”
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+