Rute 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo anthu onse ndi akulu amene anali pachipata anayankha kuti: “Ndife mboni! Yehova adalitse mkazi amene akulowa m’nyumba mwako kuti akhale ngati Rakele+ ndi Leya,+ akazi amene anabereka ana a nyumba ya Isiraeli.+ Uonetse kulemekezeka kwako mu Efurata+ ndi kudzipangira dzina m’Betelehemu.+ 1 Samueli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati bambo ako angafunse za ine, uwauze kuti, ‘Davide anandichonderera kuti ndimulole kuchoka kuti athamangire kumzinda wakwawo ku Betelehemu,+ chifukwa banja lawo lonse likukapereka nsembe ya pachaka.’+
11 Pamenepo anthu onse ndi akulu amene anali pachipata anayankha kuti: “Ndife mboni! Yehova adalitse mkazi amene akulowa m’nyumba mwako kuti akhale ngati Rakele+ ndi Leya,+ akazi amene anabereka ana a nyumba ya Isiraeli.+ Uonetse kulemekezeka kwako mu Efurata+ ndi kudzipangira dzina m’Betelehemu.+
6 Ngati bambo ako angafunse za ine, uwauze kuti, ‘Davide anandichonderera kuti ndimulole kuchoka kuti athamangire kumzinda wakwawo ku Betelehemu,+ chifukwa banja lawo lonse likukapereka nsembe ya pachaka.’+