1 Mafumu 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Patapita nthawi, Adoniya mwana wa Hagiti anapita kwa Bati-seba,+ amayi a Solomo. Iwo atamuona, anam’funsa kuti: “Kodi mwabwerera mtendere?”+ Iye anayankha kuti: “Inde, ndabwerera mtendere.” 2 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+
13 Patapita nthawi, Adoniya mwana wa Hagiti anapita kwa Bati-seba,+ amayi a Solomo. Iwo atamuona, anam’funsa kuti: “Kodi mwabwerera mtendere?”+ Iye anayankha kuti: “Inde, ndabwerera mtendere.”
22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+