1 Samueli 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano zimene zinachitika n’zakuti, pamene iwo anali kulowa, ndipo Samueli ataona Eliyabu,+ nthawi yomweyo anati: “Mosakayikira wodzozedwa wake waonekera pamaso pa Yehova.” 1 Mbiri 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Jese anabereka mwana wake woyamba Eliyabu,+ wachiwiri Abinadabu,+ wachitatu Simeya,+
6 Tsopano zimene zinachitika n’zakuti, pamene iwo anali kulowa, ndipo Samueli ataona Eliyabu,+ nthawi yomweyo anati: “Mosakayikira wodzozedwa wake waonekera pamaso pa Yehova.”