2 Samueli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Sauli anali ndi mdzakazi, dzina lake Rizipa,+ mwana wamkazi wa Aya.+ Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “N’chifukwa chiyani unagona ndi mdzakazi*+ wa bambo anga?”
7 Tsopano Sauli anali ndi mdzakazi, dzina lake Rizipa,+ mwana wamkazi wa Aya.+ Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “N’chifukwa chiyani unagona ndi mdzakazi*+ wa bambo anga?”