Salimo 18:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndidzawapera kukhala ngati fumbi louluzika ndi mphepo.+Ndidzawakhuthula ngati matope a mumsewu.+ Yesaya 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+ ndipo ndidzamulamula kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa. Ndidzamuuza+ kuti akalande zinthu zambiri, akatenge katundu wambiri, ndiponso akapondeponde anthuwo ngati matope a mumsewu.+ Mika 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani wanga adzaona zimenezi, ndipo amene anali kunena kuti: “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+ adzachita manyazi.+ Maso anga adzamuyang’ana.+ Iye adzakhala malo opondedwapondedwa ngati matope a mumsewu.+ Zekariya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+
6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+ ndipo ndidzamulamula kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa. Ndidzamuuza+ kuti akalande zinthu zambiri, akatenge katundu wambiri, ndiponso akapondeponde anthuwo ngati matope a mumsewu.+
10 Mdani wanga adzaona zimenezi, ndipo amene anali kunena kuti: “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+ adzachita manyazi.+ Maso anga adzamuyang’ana.+ Iye adzakhala malo opondedwapondedwa ngati matope a mumsewu.+
5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+