Genesis 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anapatsa Esau mkate ndi mphodza, ndipo iye anadya n’kumwa.+ Kenako, ananyamuka n’kumapita. Umu ndi mmene Esau ananyozera ukulu wake.+ 2 Samueli 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba. Ezekieli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tenga tirigu,+ balere, nyemba zikuluzikulu,+ mphodza,+ mapira, ndi tirigu wamtundu wina.*+ Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako cha masiku amene udzakhale ukugonera mbali imodzi. Udzadye chakudya chimenechi kwa masiku 390.+
34 Pamenepo Yakobo anapatsa Esau mkate ndi mphodza, ndipo iye anadya n’kumwa.+ Kenako, ananyamuka n’kumapita. Umu ndi mmene Esau ananyozera ukulu wake.+
28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.
9 “Tenga tirigu,+ balere, nyemba zikuluzikulu,+ mphodza,+ mapira, ndi tirigu wamtundu wina.*+ Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako cha masiku amene udzakhale ukugonera mbali imodzi. Udzadye chakudya chimenechi kwa masiku 390.+