Genesis 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Labani anamuuza kuti: “Ndithu, iwe ndiwe fupa langa ndi mnofu wanga.”+ Choncho anakhala naye mwezi wathunthu. Deuteronomo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu. Oweruza 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde lankhulani nzika zonse za Sekemu zikumva, kuti, ‘Chabwino n’chiti kwa inu, kuti amuna 70,+ ana onse a Yerubaala akulamulireni, kapena munthu mmodzi akulamulireni? Ndipotu kumbukirani kuti ine ndine fupa lanu ndi mnofu wanu.’”+ 2 Samueli 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu ndinu abale anga, ndinu fupa langa ndi mnofu wanga.+ Ndiye n’chifukwa chiyani inu nokha simukuchitapo kanthu kuti mfumu ibwerere?’
14 Ndiyeno Labani anamuuza kuti: “Ndithu, iwe ndiwe fupa langa ndi mnofu wanga.”+ Choncho anakhala naye mwezi wathunthu.
15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu.
2 “Chonde lankhulani nzika zonse za Sekemu zikumva, kuti, ‘Chabwino n’chiti kwa inu, kuti amuna 70,+ ana onse a Yerubaala akulamulireni, kapena munthu mmodzi akulamulireni? Ndipotu kumbukirani kuti ine ndine fupa lanu ndi mnofu wanu.’”+
12 Inu ndinu abale anga, ndinu fupa langa ndi mnofu wanga.+ Ndiye n’chifukwa chiyani inu nokha simukuchitapo kanthu kuti mfumu ibwerere?’