Genesis 43:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yosefe anawafunsa ngati ali bwino.+ Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwino? Kodi adakali ndi moyo?”+ Yesaya 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata ndi mphatso+ kwa Hezekiya atamva kuti iye anadwala koma tsopano wapezanso mphamvu.+
27 Kenako Yosefe anawafunsa ngati ali bwino.+ Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwino? Kodi adakali ndi moyo?”+
39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata ndi mphatso+ kwa Hezekiya atamva kuti iye anadwala koma tsopano wapezanso mphamvu.+