2 Samueli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense wotsala wa m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani.”+ 2 Samueli 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mfumu inauza Ziba kuti: “Taona, zonse zimene zinali za Mefiboseti+ ndi zako.” Pamenepo Ziba anati: “Ndikuwerama+ pamaso panu. Pitirizani kundikomera mtima mbuyanga mfumu.” 2 Samueli 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komabe mfumu inamuuza kuti: “N’chifukwa chiyani ukupitiriza kulankhula zonsezi? Ine ndikuti, iwe ndi Ziba mugawane mundawo.”+
9 Ndiyeno Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense wotsala wa m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani.”+
4 Kenako mfumu inauza Ziba kuti: “Taona, zonse zimene zinali za Mefiboseti+ ndi zako.” Pamenepo Ziba anati: “Ndikuwerama+ pamaso panu. Pitirizani kundikomera mtima mbuyanga mfumu.”
29 Komabe mfumu inamuuza kuti: “N’chifukwa chiyani ukupitiriza kulankhula zonsezi? Ine ndikuti, iwe ndi Ziba mugawane mundawo.”+