2 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musachitire nkhanza+ mnyamatayo Abisalomu chifukwa cha ubwino wanga.” Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleri onsewa za nkhani yokhudza Abisalomu. 2 Samueli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Yowabu anati: “Ndisachedwe chonchi ndi iwe!” Atatero anatenga mikondo itatu m’manja mwake ndi kulasa+ nayo mtima wa Abisalomu ali ndi moyo+ pakati pa mtengo waukulu.
5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musachitire nkhanza+ mnyamatayo Abisalomu chifukwa cha ubwino wanga.” Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleri onsewa za nkhani yokhudza Abisalomu.
14 Pamenepo Yowabu anati: “Ndisachedwe chonchi ndi iwe!” Atatero anatenga mikondo itatu m’manja mwake ndi kulasa+ nayo mtima wa Abisalomu ali ndi moyo+ pakati pa mtengo waukulu.