2 Samueli 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi. 2 Samueli 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mfumu inauza Zadoki kuti: “Tenga likasa+ la Mulungu woona ndi kubwerera nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandibwezeretsa mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+ 1 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.
17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi.
25 Ndiyeno mfumu inauza Zadoki kuti: “Tenga likasa+ la Mulungu woona ndi kubwerera nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandibwezeretsa mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+
8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.