2 Samueli 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mwamuna wake anali kumutsatira. Iye anali kumutsatira pambuyo akulira mpaka kukafika ku Bahurimu.+ Kenako Abineri anamuuza kuti: “Bwerera!” Pamenepo iye anabwerera. 2 Samueli 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komabe mnyamata wina anawaona ndipo anapita kukauza Abisalomu. Choncho awiriwo anachoka mofulumira ndi kupita kunyumba ya munthu wina amene anali ndi chitsime pakhomo pake ku Bahurimu,+ ndipo iwo analowa m’chitsimemo.
16 Koma mwamuna wake anali kumutsatira. Iye anali kumutsatira pambuyo akulira mpaka kukafika ku Bahurimu.+ Kenako Abineri anamuuza kuti: “Bwerera!” Pamenepo iye anabwerera.
18 Komabe mnyamata wina anawaona ndipo anapita kukauza Abisalomu. Choncho awiriwo anachoka mofulumira ndi kupita kunyumba ya munthu wina amene anali ndi chitsime pakhomo pake ku Bahurimu,+ ndipo iwo analowa m’chitsimemo.