Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+

  • 2 Samueli 17:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Komabe mnyamata wina anawaona ndipo anapita kukauza Abisalomu. Choncho awiriwo anachoka mofulumira ndi kupita kunyumba ya munthu wina amene anali ndi chitsime pakhomo pake ku Bahurimu,+ ndipo iwo analowa m’chitsimemo.

  • 1 Mafumu 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Taona, ukukhala pafupi ndi Simeyi+ wa ku Bahurimu,+ mwana wa Gera M’benjamini. Iyeyu ananditemberera temberero lopweteka+ tsiku limene ndinkapita ku Mahanaimu.+ Ndi iyeyu amene anabwera kudzakumana nane pa Yorodano,+ choncho ndinamulumbirira pamaso pa Yehova kuti: ‘Sindidzakupha ndi lupanga.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena