2 Samueli 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuchokera tsiku limene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzakupatsa mpumulo kwa adani ako onse.+ “‘“Tsopano Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira banja lachifumu.+ 1 Mbiri 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ngati mmene anachitira kuchokera masiku amene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndipo ndidzatsitsa adani ako onse.+ Tsopano ndikukuuza kuti: ‘Kuwonjezera pamenepo, Yehova adzakumangira nyumba.’*+ Salimo 89:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma kukoma mtima kwanga kosatha sindidzakuchotsa pa iye,+Ndipo sindidzasiya kukhulupirika kwanga.+
11 kuchokera tsiku limene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzakupatsa mpumulo kwa adani ako onse.+ “‘“Tsopano Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira banja lachifumu.+
10 ngati mmene anachitira kuchokera masiku amene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndipo ndidzatsitsa adani ako onse.+ Tsopano ndikukuuza kuti: ‘Kuwonjezera pamenepo, Yehova adzakumangira nyumba.’*+
33 Koma kukoma mtima kwanga kosatha sindidzakuchotsa pa iye,+Ndipo sindidzasiya kukhulupirika kwanga.+