Levitiko 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+ Numeri 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7,+ muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Muzichita chikondwerero kwa Yehova masiku 7.+ 1 Mafumu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho anthu onse a mu Isiraeli anasonkhana kwa Mfumu Solomo pachikondwerero+ cha m’mwezi wa Etanimu, womwe ndi mwezi wa 7.+
34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+
12 “‘Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7,+ muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Muzichita chikondwerero kwa Yehova masiku 7.+
2 Choncho anthu onse a mu Isiraeli anasonkhana kwa Mfumu Solomo pachikondwerero+ cha m’mwezi wa Etanimu, womwe ndi mwezi wa 7.+