1 Samueli 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Patapita nthawi, Samueli+ anamwalira ndipo Aisiraeli onse anasonkhana pamodzi ndi kulira+ maliro ake. Iwo anamuika m’manda panyumba yake ku Rama.+ Kenako Davide ananyamuka ndi kupita kuchipululu cha Parana.+
25 Patapita nthawi, Samueli+ anamwalira ndipo Aisiraeli onse anasonkhana pamodzi ndi kulira+ maliro ake. Iwo anamuika m’manda panyumba yake ku Rama.+ Kenako Davide ananyamuka ndi kupita kuchipululu cha Parana.+