2 Mbiri 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa chakuti Rehobowamu anadzichepetsa, Yehova anabweza mkwiyo wake+ ndipo sanaganizenso zoti awawononge anthu onsewo.+ Komanso mwa anthu a ku Yuda munapezeka ntchito zabwino.+ Ezekieli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Ndiyeno munthu wina wabereka mwana wamwamuna amene amaona machimo onse amene bambo ake amachita. Mwanayo amaona machimowo koma sawachita.+
12 Chifukwa chakuti Rehobowamu anadzichepetsa, Yehova anabweza mkwiyo wake+ ndipo sanaganizenso zoti awawononge anthu onsewo.+ Komanso mwa anthu a ku Yuda munapezeka ntchito zabwino.+
14 “‘Ndiyeno munthu wina wabereka mwana wamwamuna amene amaona machimo onse amene bambo ake amachita. Mwanayo amaona machimowo koma sawachita.+