Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Bwanji ngati mumzindamo mutapezeka anthu olungama 50, kodi muwawonongabe? Kodi simukhululukira mzindawo chifukwa cha olungama 50 amenewo?+

  • 1 Mafumu 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipo Aisiraeli onse akamulira+ ndi kumuika m’manda. Iwo akamulira popeza m’banja lonse la Yerobowamu, uyu yekha ndiye adzaikidwe m’manda chifukwa chakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli, wapeza chinachake chabwino mwa yekhayu m’nyumba yonse ya Yerobowamu.+

  • 2 Mbiri 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena