1 Mafumu 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kenako Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ bambo ake. Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mbiri 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ufumu wa Rehobowamu utangokhazikika+ ndiponso iye atangokhala wamphamvu, iye ndi Aisiraeli onse+ anasiya chilamulo cha Yehova.+
43 Kenako Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ bambo ake. Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.
12 Ufumu wa Rehobowamu utangokhazikika+ ndiponso iye atangokhala wamphamvu, iye ndi Aisiraeli onse+ anasiya chilamulo cha Yehova.+