Ekisodo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+ 1 Mafumu 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wawo amene anatulutsa makolo awo m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake, anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira. N’chifukwa chake Yehova anawabweretsera tsoka lonseli.’”+ Yeremiya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’
4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+
9 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wawo amene anatulutsa makolo awo m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake, anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira. N’chifukwa chake Yehova anawabweretsera tsoka lonseli.’”+
13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’