Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 ndipo moto unatsika kuchokera kwa Yehova+ n’kunyeketsa nsembe yopsereza ndiponso mafuta, zimene zinali paguwa lansembe. Anthu onse ataona zimenezi, anayamba kufuula mokondwera+ ndipo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.

  • Oweruza 6:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Atatero, mngelo wa Yehova anatambasula dzanja lake, ndipo anakhudza nyama ndi mikate yopanda chofufumitsayo ndi nsonga ya ndodo imene inali m’dzanja lake. Pamenepo, moto wotuluka m’mwalawo unayamba kulilima, n’kunyeketsa nyama ndi mkate wopanda chofufumitsawo,+ koma mngelo wa Yehova anazimiririka.

  • 1 Mbiri 21:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiyeno Davide anamangira Yehova guwa lansembe pamalopo,+ ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Komanso anaitana pa dzina la Yehova+ yemwe tsopano anamuyankha ndi moto+ wochokera kumwamba umene unafika paguwa lansembe yopsereza.

  • 2 Mbiri 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera,+ moto unatsika kuchokera kumwamba.+ Motowo unanyeketsa nsembe yopsereza+ pamodzi ndi nsembe zina, ndipo ulemerero wa Yehova+ unadzaza nyumbayo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena