Yesaya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+ Aroma 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma kodi mawu a Mulungu+ anati chiyani kwa iyeyo? Anati: “Ndadzisungira anthu 7,000, amene sanagwadire Baala.”+ Aroma 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero, pa nthawi ino alipo ena ochepa+ amene anasankhidwa+ mwa kukoma mtima kwakukulu. 2 Timoteyo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komabe, maziko olimba a Mulungu adakali chikhalire,+ ndipo ali ndi chidindo cha mawu akuti: “Yehova* amadziwa anthu ake,”+ ndiponso akuti: “Aliyense wotchula dzina la Yehova+ aleke kuchita zosalungama.”+
9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+
4 Koma kodi mawu a Mulungu+ anati chiyani kwa iyeyo? Anati: “Ndadzisungira anthu 7,000, amene sanagwadire Baala.”+
19 Komabe, maziko olimba a Mulungu adakali chikhalire,+ ndipo ali ndi chidindo cha mawu akuti: “Yehova* amadziwa anthu ake,”+ ndiponso akuti: “Aliyense wotchula dzina la Yehova+ aleke kuchita zosalungama.”+