Yesaya 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova Mulungu wathu, ife takhalapo m’manja mwa ambuye ena kupatula inu.+ Koma chifukwa cha thandizo lanu, timatha kutchula dzina lanu.+ Zefaniya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo ndidzapatsa mitundu ya anthu chilankhulo choyera+ kuti onse aziitanira pa dzina la Yehova+ ndi kumutumikira mogwirizana.’*+ Zefaniya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+
13 Inu Yehova Mulungu wathu, ife takhalapo m’manja mwa ambuye ena kupatula inu.+ Koma chifukwa cha thandizo lanu, timatha kutchula dzina lanu.+
9 Pamenepo ndidzapatsa mitundu ya anthu chilankhulo choyera+ kuti onse aziitanira pa dzina la Yehova+ ndi kumutumikira mogwirizana.’*+
12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+