2 Samueli 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patapita zaka ziwiri zathunthu, anthu ena anali kumeta ubweya wa nkhosa+ za Abisalomu ku Baala-hazori, pafupi ndi Efuraimu.+ Choncho Abisalomu anaitanira ana onse aamuna a mfumu kumeneko.+
23 Patapita zaka ziwiri zathunthu, anthu ena anali kumeta ubweya wa nkhosa+ za Abisalomu ku Baala-hazori, pafupi ndi Efuraimu.+ Choncho Abisalomu anaitanira ana onse aamuna a mfumu kumeneko.+