Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pomaliza Adoniya anapereka nsembe+ za nkhosa, ng’ombe, ndi ana a ng’ombe onenepa pafupi ndi mwala wa Zoheleti umene uli pafupi ndi Eni-rogeli.+ Kumeneko anaitanirako abale ake onse, omwe anali ana a mfumu,+ ndi amuna onse a mu Yuda, omwe anali atumiki a mfumu.

  • 1 Mafumu 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iye wapereka nsembe zambiri, za ng’ombe zamphongo, ana a ng’ombe onenepa, ndiponso nkhosa. Waitananso ana onse a mfumu,+ wansembe Abiyatara,+ ndi Yowabu+ mkulu wa asilikali, koma Solomo mtumiki wanu sanamuitane.+

  • 1 Mafumu 1:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Chifukwatu lero wapita kukapereka nsembe+ zambiri, za ng’ombe zamphongo, ana a ng’ombe onenepa, ndi nkhosa. Waitananso ana onse a mfumu, akulu a asilikali ndi wansembe Abiyatara.+ Moti panopa ali kumeneko ndipo akudya ndi kumwa pamaso pake n’kumanena kuti, ‘Mfumu Adoniya ikhale ndi moyo wautali!’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena