Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kenako Mulungu anati: “M’madzi mukhale zamoyo zambirimbiri,+ ndiponso zolengedwa zouluka ziuluke m’mlengalenga mwa dziko lapansi.”+

  • Yobu 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Koma funsa nyama zoweta ndipo zikulangiza.+

      Komanso zouluka zam’mlengalenga, ndipo zikuuza.+

  • Miyambo 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Iye akulondola mkaziyo mpaka muvi utaboola chiwindi* chake,+ ngati mbalame yothamangira kumsampha,+ ndipo iye sakudziwa kuti zikukhudza moyo wake.+

  • Miyambo 30:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Njira ya chiwombankhanga m’mlengalenga, njira ya njoka pamwala, njira ya ngalawa pakatikati pa nyanja,+ ndiponso njira ya mwamuna ndi mtsikana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena