1 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+ Miyambo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+ Miyambo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana amakhala wanzeru ngati akulandira malangizo* kuchokera kwa bambo ake.+ Koma amene sanamve chidzudzulo amakhala wonyoza.+ Miyambo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanzeru ndi amene amakondweretsa bambo ake,+ koma wopusa amanyoza mayi ake.+ Miyambo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Bambo wa munthu wolungama ndithu adzasangalala.+ Bambo wobereka mwana wanzeru adzakondwera naye.+
9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+
10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+
13 Mwana amakhala wanzeru ngati akulandira malangizo* kuchokera kwa bambo ake.+ Koma amene sanamve chidzudzulo amakhala wonyoza.+