-
1 Mbiri 28:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tsopano mwaima pamaso pa Aisiraeli onse, amene ndi mpingo wa Yehova,+ ndiponso Mulungu wathu akumva zimenezi.+ Choncho samalani ndi kutsatira malamulo onse a Yehova Mulungu wanu, kuti dziko labwinoli+ likhale lanu ndi kuti mudzasiyire ana anu obwera pambuyo panu monga cholowa chawo mpaka kalekale.
-
-
2 Mbiri 6:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Tsopano inu Yehova Mulungu wa Isiraeli, sungani lonjezo limene munalonjeza mtumiki wanu Davide bambo anga lakuti, ‘Anthu a m’banja lako sadzasiya kukhala pamaso panga pampando wachifumu wa Isiraeli.+ Chofunika n’choti ana ako+ asamale mayendedwe awo mwa kuyenda motsatira malamulo anga+ monga momwe iwe wayendera pamaso panga.’+
-