Salimo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+ Salimo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+ Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+
2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+
17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+ Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+