Levitiko 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mukapewa kuchita zimenezi, dziko silidzakusanzani chifukwa choliipitsa mmene lidzasanzira mitundu imene ikukhalamo musanafike inu.+ Deuteronomo 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+ 2 Mafumu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 mpaka Yehova anachotsa Isiraeli pamaso pake+ monga momwe ananenera kudzera mwa atumiki ake onse, aneneri.+ Choncho Isiraeli anachoka m’dziko lake n’kupita ku Asuri, ndipo ali komweko mpaka lero.+
28 Mukapewa kuchita zimenezi, dziko silidzakusanzani chifukwa choliipitsa mmene lidzasanzira mitundu imene ikukhalamo musanafike inu.+
26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+
23 mpaka Yehova anachotsa Isiraeli pamaso pake+ monga momwe ananenera kudzera mwa atumiki ake onse, aneneri.+ Choncho Isiraeli anachoka m’dziko lake n’kupita ku Asuri, ndipo ali komweko mpaka lero.+