Yoswa 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Apa m’pamene Horamu mfumu ya ku Gezeri+ anapita kukathandiza mzinda wa Lakisi. Koma Yoswa anapha Horamu ndi anthu ake onse, moti sipanatsale wopulumuka.+ Oweruza 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Fuko la Efuraimu nalonso silinapitikitse Akanani amene anali kukhala ku Gezeri, moti Akananiwo anakhalabe pakati pawo ku Gezeriko.+
33 Apa m’pamene Horamu mfumu ya ku Gezeri+ anapita kukathandiza mzinda wa Lakisi. Koma Yoswa anapha Horamu ndi anthu ake onse, moti sipanatsale wopulumuka.+
29 Fuko la Efuraimu nalonso silinapitikitse Akanani amene anali kukhala ku Gezeri, moti Akananiwo anakhalabe pakati pawo ku Gezeriko.+