6 Patapita nthawi, ana a Amoni anaona kuti akhala chinthu chonunkha+ kwa Davide. Choncho Hanuni+ ndi ana a Amoni anatumiza matalente asiliva 1,000+ kuti akabwereke magaleta+ ndi kulemba ganyu asilikali okwera pamahatchi a ku Mesopotamiya, a ku Aramu-maaka+ ndi a ku Zoba.+