1 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Palibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta, ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta, ndi a amuna ake okwera pamahatchi.+ 2 Mbiri 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anali mtumiki+ wa Solomo mwana wa Davide, anapanduka+ n’kuukira mbuye wake.+
22 Palibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta, ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta, ndi a amuna ake okwera pamahatchi.+
6 Koma Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anali mtumiki+ wa Solomo mwana wa Davide, anapanduka+ n’kuukira mbuye wake.+