Yesaya 41:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Anthu ozunzika ndi osauka akufunafuna madzi,+ koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma ndi ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+
17 “Anthu ozunzika ndi osauka akufunafuna madzi,+ koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma ndi ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+