Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 63:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+

      Moyo wanga ukulakalaka inu.+

      Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inu

      M’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+

  • Yesaya 55:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.+ Inde bwerani mudzagule vinyo+ ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo wake.+

  • Amosi 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera pamene ndidzatumiza njala m’dziko. Njala imeneyo siidzakhala ya chakudya kapenanso ludzu lofuna madzi ayi, koma idzakhala njala ndiponso ludzu lofuna kumva mawu a Yehova.+

  • Chivumbulutso 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mzimu+ ndi mkwatibwi+ akunenabe kuti: “Bwera!” Aliyense wakumva anene kuti: “Bwera!”+ Aliyense wakumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi a moyo kwaulere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena