Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 kuti, ‘Mverani Aisiraeli inu. Lero mukuyandikira adani anu kuti mumenyane nawo. Mitima yanu isachite mantha.+ Musaope ndipo musathawe mwamantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,+

  • Yesaya 41:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+

  • Yesaya 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena